Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 78:59 - Buku Lopatulika

59 Pakumva ichi Mulungu, anakwiya, nanyozatu Israele;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

59 Pakumva ichi Mulungu, anakwiya, nanyozatu Israele;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

59 Pamene Mulungu adamva zimenezi, adakwiya kwambiri, ndipo adakana Aisraele kotheratu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

59 Pamene Mulungu anamva zimenezi, anakwiya kwambiri; Iye anakana Israeli kwathunthu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:59
9 Mawu Ofanana  

Potero udayaka mkwiyo wa Yehova pa anthu ake, nanyansidwa Iye ndi cholowa chake.


Yehova ali mu Kachisi wake woyera, Yehova, mpando wachifumu wake uli mu Mwamba; apenyerera ndi maso ake, ayesa ana a anthu ndi zikope zake.


Ambuye wataya guwa lake la nsembe, malo ake opatulika amnyansira; wapereka m'manja a adani ake makoma a zinyumba zake; iwo anapokosera m'nyumba ya Yehova ngati tsiku la msonkhano.


Musamatsata miyambo ya mtundu umene ndiuchotsa pamaso panu; popeza anachita izi zonse, ndinalema nao.


Ndiponso pali ichinso: pokhala iwo m'dziko la adani ao sindidzawakaniza, kapena kunyansidwa nao, kuwaononga konse, ndi kuthyola pangano langa ndinapangana nao; popeza Ine ndine Yehova Mulungu wao.


Ndipo ndinatha abusa atatuwo mwezi umodzi; pakuti mtima wanga unalema nao, ndi mtima waonso unaipidwa nane.


Ndipo Yehova anachiona, nawanyoza, pakuipidwa nao ana ake aamuna, ndi akazi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa