Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 78:48 - Buku Lopatulika

48 Naperekanso zoweta zao kwa matalala, ndi ng'ombe zao kwa mphezi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

48 Naperekanso zoweta zao kwa matalala, ndi ng'ombe zao kwa mphezi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

48 Adalola kuti ng'ombe zao zife ndi matalala ndi kuti nkhosa zao zife ndi zing'aning'ani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

48 Iye anapereka ngʼombe zawo ku matalala, zoweta zawo ku zingʼaningʼani.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:48
3 Mawu Ofanana  

Ndipo tsopano, tumiza, thawitsa zoweta zako ndi zonse uli nazo pabwalo; pakuti anthu onse ndi zoweta zonse zopezeka pabwalo, zosasonkhanidwa m'nyumba, matalala adzazigwera, ndipo zidzafa.


Ndipo matalala anapanda m'dziko lonse la Ejipito zonse za pabwalo, kuyambira anthu kufikira zoweta; ndipo matalala anapanda zitsamba zonse zakuthengo, nathyola mitengo yonse yakuthengo.


Pembani kwa Yehova; chifukwa akwanira ndithu mabingu a Mulungu ndi matalala; ndipo ndidzakulolani mumuke, osakhalanso.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa