Masalimo 78:47 - Buku Lopatulika47 Anapha mphesa zao ndi matalala, ndi mikuyu yao ndi chisanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 Anapha mphesa zao ndi matalala, ndi mikuyu yao ndi chisanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 Adaononga mphesa zao ndi matalala ndiponso mitengo yao yankhuyu ndi chisanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 Iye anawononga mphesa zawo ndi matalala ndiponso mitengo yawo yankhuyu ndi chisanu. Onani mutuwo |