Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 78:39 - Buku Lopatulika

39 Ndipo anakumbukira kuti iwo ndiwo anthu; mphepo yopita yosabweranso.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

39 Ndipo anakumbukira kuti iwo ndiwo anthu; mphepo yopita yosabweranso.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

39 Ankakumbukira kuti iwo anali anthu chabe, ngati mphepo yopita imene siibwereranso.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

39 Iye anakumbukira kuti iwo anali anthu chabe, mphepo yopita imene sibwereranso.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:39
7 Mawu Ofanana  

Ndipo anati Yehova, Mzimu wanga sudzakangana ndi anthu nthawi zonse, chifukwa iwonso ndiwo thupi lanyama: koma masiku ake adzakhala zaka zana limodzi kudza makumi awiri.


Mukumbukire kuti mwandiumba ngati dothi; ndipo kodi mudzandibwezera kufumbi?


Ndinyansidwa nao moyo wanga; sindidzakhala ndi moyo chikhalire; mundileke; pakuti masiku anga ndi achabe.


Kumbukira kuti moyo wanga ndiwo mphepo, diso langa silidzaonanso chokoma.


Chobadwa m'thupi chikhala thupi, ndipo chobadwa mwa Mzimu, chikhala mzimu.


inu amene simudziwa chimene chidzagwa mawa. Moyo wanu uli wotani? Pakuti muli utsi, wakuonekera kanthawi, ndi pamenepo ukanganuka.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa