Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 78:34 - Buku Lopatulika

34 Pamene anawapha ndipo anamfuna Iye; nabwerera, nafunitsitsa Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

34 Pamene anawapha ndipo anamfuna Iye; nabwerera, nafunitsitsa Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

34 Pamene ankapha ena, otsalira ankayamba kumufunafuna. Ankalapa namafunafuna Mulungu ndi mtima wao wonse.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

34 Mulungu atawapha, iwo amamufunafuna Iyeyo; iwo ankatembenukiranso kwa Iye mwachangu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:34
10 Mawu Ofanana  

Yehova, iwo adza kwa Inu movutika, iwo anathira pemphero, muja munalikuwalanga.


Phazi lidzaupondereza pansi; ngakhale mapazi a aumphawi, ndi mapondedwe a osowa.


Iwe wokhala mu Lebanoni, womanga chisa chako m'mikungudza, udzachitidwa chisoni chachikulu nanga pamene mapweteko adzadza kwa iwe, monga mkazi alinkudwala!


Ndidzamuka ndi kubwerera kunka kumalo kwanga, mpaka adzavomereza kupalamula kwao, nafunafuna nkhope yanga; m'msauko mwao adzandifunafuna mwachangu.


Ndipo sanafuulire kwa Ine ndi mtima wao, koma alira pakama pao, asonkhanira tirigu ndi vinyo, apikisana ndi Ine.


Ndipo anthu anadza kwa Mose, nati, Tachimwa, popeza tinanena motsutsana ndi Yehova, ndi inu; pempherani kwa Yehova kuti atichotsere njokazi. Ndipo Mose anawapempherera anthu.


Ndipo ana a Israele anafuula kwa Yehova; pakuti anali nao magaleta achitsulo mazana asanu ndi anai; napsinja ana a Israele kolimba zaka makumi awiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa