Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 78:32 - Buku Lopatulika

32 Chingakhale ichi chonse anachimwanso, osavomereza zodabwitsa zake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 Chingakhale ichi chonse anachimwanso, osavomereza zodabwitsa zake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Ngakhale zinali chomwecho, iwo adapitirirabe kuchimwa, sadakhulupirire ngakhale adaona zodabwitsa zake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Ngakhale zinali chomwechi, iwo anapitirira kuchimwa; ngakhale anaona zozizwitsa zakezo iwowo sanakhulupirirebe.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:32
9 Mawu Ofanana  

Ndipo anaiwala zochita Iye, ndi zodabwitsa zake zimene anawaonetsa.


Popeza sanakhulupirire Mulungu, osatama chipulumutso chake.


Koma nyumba ya Israele inapandukira Ine m'chipululu, sanayende m'malemba anga, nanyoza maweruzo anga, amene munthu akawachita adzakhala nao ndi moyo; ndi masabata anga anawaipsa kwambiri; pamenepo ndidati ndiwatsanulire ukali wanga m'chipululu kuwatha.


Koma anati kwa iye, Ngati samvera Mose ndi aneneri, sadzakopeka mtima ngakhale wina akauka kwa akufa.


Koma angakhale adachita zizindikiro zambiri zotere pamaso pao iwo sanakhulupirire Iye;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa