Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 78:31 - Buku Lopatulika

31 pamenepo mkwiyo wa Mulungu unawaukira, ndipo anapha mwa onenepa ao, nagwetsa osankhika a Israele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

31 pamenepo mkwiyo wa Mulungu unawaukira, ndipo anapha mwa onenepa ao, nagwetsa osankhika a Israele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

31 mkwiyo wa Mulungu udaŵayakira, ndipo adapha amphamvu onse pakati pao, adapha anyamata abwinoabwino onse a mu Israele.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

31 mkwiyo wa Mulungu unawayakira; Iye anapha amphamvu onse pakati pawo, kugwetsa anyamata abwino kwambiri mu Israeli.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:31
2 Mawu Ofanana  

Chifukwa chake Ambuye, Yehova wa makamu, adzatumiza kuonda mwa onenepa ake; ndipo pansi pa ulemerero wake padzayaka kutentha, konga ngati kutentha kwa moto.


Nyamayi ikali pakati pa mano, asanaitafune, Mulungu anapsa mtima pa anthuwa, ndipo Yehova anawakantha anthu ndi kukantha kwakukulu ndithu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa