Masalimo 78:29 - Buku Lopatulika29 Potero anadya nakhuta kwambiri; ndipo anawapatsa chokhumba iwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Potero anadya nakhuta kwambiri; ndipo anawapatsa chokhumba iwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Motero adadya nakhuta kwambiri, popeza kuti adaŵapatsa zakudya zimene ankakhumba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Iwo anadya mpaka anatsala nazo zochuluka pakuti Iye anawapatsa zimene anazilakalaka. Onani mutuwo |