Masalimo 78:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo anawavumbitsira nyama ngati fumbi, ndi mbalame zouluka ngati mchenga wa kunyanja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo anawavumbitsira nyama ngati fumbi, ndi mbalame zouluka ngati mchenga wa kunyanja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Adaŵagwetsera nyama yochuluka ngati fumbi, mbalame zochuluka ngati mchenga wakunyanja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Iye anawagwetsera nyama ngati fumbi, mbalame zowuluka ngati mchenga wa mʼmbali mwa nyanja. Onani mutuwo |