Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 78:25 - Buku Lopatulika

25 Yense anadya mkate wa angelo, anawatumizira chakudya chofikira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

25 Yense anadya mkate wa angelo, anawatumizira chakudya chofikira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

25 Motero anthu adadya buledi wa angelo, ndipo Mulungu adaŵatumizira chakudya chochuluka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

25 Anthu anadya buledi wa angelo, Iye anawatumizira chakudya chonse chimene akanatha kudya.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:25
5 Mawu Ofanana  

Lemekezani Yehova, inu angelo ake; a mphamvu zolimba, akuchita mau ake, akumvera liu la mau ake.


Anafunsa ndipo Iye anadzetsa zinziri, nawakhutitsa mkate wakumwamba.


Nanenanso Mose, Pakukupatsani Yehova nyama ya kudya madzulo, ndi mkate wokhuta m'mawa, atero popeza Yehova adamva madandaulo anu amene mumdandaulira nao. Koma ife ndife chiyani? Simulikudandaulira ife koma Yehova.


Ndipo anadya onse, nakhuta; ndipo anatola makombo otsala, nadzala madengu khumi ndi iwiri.


Ndipo onsewa anadya, nakhuta: ndipo anatola makombo otsala madengu asanu ndi awiri odzala.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa