Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 78:22 - Buku Lopatulika

22 Popeza sanakhulupirire Mulungu, osatama chipulumutso chake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Popeza sanakhulupirire Mulungu, osatama chipulumutso chake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 popeza kuti sadadalire Mulungu, sadakhulupirire mphamvu zake zopulumutsa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 pakuti iwo sanakhulupirire Mulungu kapena kudalira chipulumutso chake.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:22
10 Mawu Ofanana  

Koma sanamvere, naumitsa khosi lao, monga khosi la makolo ao amene sanakhulupirire Yehova Mulungu wao.


Anapeputsanso dziko lofunika, osavomereza mau ake;


ndipo mutu wa Efuremu ndi Samariya, ndi mutu wa Samariya ndi mwana wa Remaliya, mukapanda kukhulupirira ndithu simudzakhazikika.


Sanamvera mau, sanalole kulangizidwa; sanakhulupirire Yehova, sanayandikire kwa Mulungu wake.


Koma m'chinthu ichi simunakhulupirire Yehova Mulungu wanu,


koma wopanda chikhulupiriro sikutheka kumkondweretsa; pakuti iye wakudza kwa Mulungu ayenera kukhulupirira kuti alipo, ndi kuti ali wobwezera mphotho iwo akumfuna Iye.


Tapenyani, abale, kuti kapena ukakhale mwa wina wa inu mtima woipa wosakhulupirira, wakulekana ndi Mulungu wamoyo;


Iye amene amkhulupirira Mwana wa Mulungu ali nao umboni mwa iye; iye wosakhulupirira Mulungu anamuyesa Iye wonama; chifukwa sanakhulupirire umboni wa Mulungu anauchita wa Mwana wake.


Koma ndifuna kukukumbutsani mungakhale munadziwa zonse kale, kuti Ambuye, atapulumutsa mtundu wa anthu ndi kuwatulutsa m'dziko la Ejipito, anaononganso iwo osakhulupirira.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa