Masalimo 78:20 - Buku Lopatulika20 Taonani, anapanda thanthwe, ndi madzi anayendako ndi mitsinje inasefuka; kodi adzakhozanso kupatsa mkate? Kodi adzafunira anthu ake nyama? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Taonani, anapanda thanthwe, ndi madzi anayendako ndi mitsinje inasefuka; kodi adzakhozanso kupatsa mkate? Kodi adzafunira anthu ake nyama? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Paja adamenya thanthwe, kotero kuti madzi adatumphuka, ndipo mitsinje idadzaza. Kodi angathenso kutipatsa ife anthu ake buledi kapena kutipezera nyama?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Iye atamenya thanthwe madzi anatuluka, ndipo mitsinje inadzaza ndi madzi. Koma iye angatipatsenso ife chakudya? Kodi angapereke nyama kwa anthu akewa?” Onani mutuwo |