Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 78:14 - Buku Lopatulika

14 Ndipo msana anawatsogolera ndi mtambo ndi usiku wonse ndi kuunika kwa moto.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Ndipo msana anawatsogolera ndi mtambo ndi usiku wonse ndi kuunika kwa moto.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Masana ankaŵatsogolera ndi mitambo, usiku ankaŵatsogolera ndi kuŵala kwamoto.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Anawatsogolera ndi mtambo masana ndi kuwala kwa moto usiku wonse.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 78:14
8 Mawu Ofanana  

Munawatsogoleranso usana ndi mtambo woti njo, ndi moto tolo usiku, kuwaunikira m'njira akayendamo.


koma Inu mwa nsoni zanu zazikulu simunawasiye m'chipululu; mtambo woti njo sunawachokere usana kuwatsogolera m'njira, ngakhale moto wa tolo usiku kuwaunikira panjira anayenera kuyendamo.


Anayala mtambo uwaphimbe; ndi moto uunikire usiku.


Ndipo kunali, ulonda wa mamawa, Yehova ali m'moto ndi m'mtambo njo anapenyera pa ulendo wa Aejipito, nauvuta ulendo wa Aejipito.


Kudatero kosalekeza; mtambo umachiphimba, ndi moto umaoneka usiku.


ndi chimene anakuchitirani m'chipululu, kufikira munadza kumalo kuno;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa