Masalimo 77:19 - Buku Lopatulika19 Njira yanu inali m'nyanja, koyenda Inu nkumadzi aakulu, ndipo mapazi anu sanadziwike. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Njira yanu inali m'nyanja, koyenda Inu nku madzi aakulu, ndipo mapazi anu sanadziwike. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Inu mudadzera pa nyanja, njira yanu idadzera pa madzi akuya, komabe mapazi anu sadaoneke. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Njira yanu inadutsa pa nyanja, njira yanu inadutsa pa madzi amphamvu, ngakhale zidindo za mapazi anu sizinaoneke. Onani mutuwo |