Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 77:16 - Buku Lopatulika

16 Madziwo anakuonani Mulungu; anakuonani madziwo; anachita mantha, zozama zomwe zinanjenjemera.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Madziwo anakuonani Mulungu; anakuonani madziwo; anachita mantha, zozama zomwe zinanjenjemera.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Pamene madzi adakuwonani, Inu Mulungu, pamene madzi adakuwonani, adachita mantha, inde, nyanja yakuya idanjenjemera.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Madzi anakuonani Mulungu, madzi anakuonani ndipo anachita mantha; nyanja yozama inakomoka.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 77:16
7 Mawu Ofanana  

Tsopano ana ako aamuna awiri, amene anakubadwira iwe m'dziko la Ejipito, ndisanadze kwa iwe ku Ejipito, ndiwo anga; Efuremu ndi Manase, monga Rubeni ndi Simeoni, ndiwo anga.


Ndipo Mose anatambasulira dzanja lake kunyanja; ndipo Yehova anabweza nyanja ndi mphepo yolimba ya kum'mawa usiku wonse, naumitsa nyanja; ndipo madziwo anagawikana.


Chifukwa chake nena kwa ana a Israele Ine ndine Yehova, ndipo ndidzakutulutsani pansi pa akatundu a Aejipito ndipo ndidzakulanditsani ku ukapolo wanu; ndipo ndidzakuombolani ndi dzanja lotambasuka, ndi maweruzo aakulu;


Munaponda panyanja ndi akavalo anu, madzi amphamvu anaunjikana mulu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa