Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 77:13 - Buku Lopatulika

13 Mulungu, m'malo opatulika muli njira yanu; Mulungu wamkulu ndani monga Mulungu?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

13 Mulungu, m'malo opatulika muli njira yanu; Mulungu wamkulu ndani monga Mulungu?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

13 Njira zanu, Inu Mulungu, nzoyera. Kodi alipo mulungu winanso wamkulu ngati Mulungu wathu?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

13 Njira zanu Mulungu ndi zoyera. Kodi ndi mulungu uti ali wamkulu kuposa Mulungu wathu?

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 77:13
14 Mawu Ofanana  

Muimbireni, muimbireni zomlemekeza; fotokozerani zodabwitsa zake zonse.


Mundizindikiritse njira ya malangizo anu; kuti ndilingalire zodabwitsa zanu.


Chinthu chimodzi ndinachipempha kwa Yehova, ndidzachilondola ichi, Kuti ndikhalitse m'nyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga, kupenya kukongola kwake kwa Yehova ndi kufunsitsa mu Kachisi wake.


Kuti ndione mphamvu yanu ndi ulemerero wanu, monga ndinakuonani m'malo oyera.


Oimbira anatsogolera, oimba zoimba anatsata m'mbuyo, pakatipo anamwali oimba mangaka.


Chilungamo chanunso, Mulungu, chifikira kuthambo; Inu amene munachita zazikulu, akunga Inu ndani, Mulungu?


mpaka ndinalowa m'zoyera za Mulungu, ndi kulingalira chitsiriziro chao.


Pakati pa milungu palibe wina wonga Inu, Ambuye; ndipo palibe ntchito zonga zanu.


Afanana ndi Inu ndani mwa milungu, Yehova? Afanana ndi Inu ndani, wolemekezedwa, woyera, woopsa pomyamika, wakuchita zozizwa?


Mudzafanizira Mulungu ndi yani tsopano, kapena kumyerekeza ndi chithunzithunzi chotani?


Mudzandifanizira Ine ndi yani tsono, kuti ndilingane naye, ati Woyerayo.


Kodi mudzandifanizira ndi yani, ndi kundilinganiza ndi kundiyerekeza, kuti ife tifanane?


Popeza thanthwe lao nlosanga Thanthwe lathu, oweruza a pamenepo ndiwo adani athu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa