Masalimo 77:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo ndidzalingalira ntchito yanu yonse, ndi kulingalirabe zimene munazichita Inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo ndidzalingalira ntchito yanu yonse, ndi kulingalirabe zimene munazichita Inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Ndidzasinkhasinkha za zonse zimene mwachita, ndidzalingalira za ntchito zanu zamphamvuzo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ndidzakumbukira ntchito zanu ndi kulingalira zodabwitsa zanu.” Onani mutuwo |