Masalimo 75:9 - Buku Lopatulika9 Koma ine ndidzalalikira kosalekeza, ndidzaimbira zomlemekeza Mulungu wa Yakobo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Koma ine ndidzalalikira kosalekeza, ndidzaimbira zomlemekeza Mulungu wa Yakobo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Koma ine sindidzaleka kukondwera, ndidzaimba nyimbo zotamanda Mulungu wa Yakobe mpaka muyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Kunena za ine, ndidzalengeza izi kwamuyaya; ndidzayimba matamando kwa Mulungu wa Yakobo. Onani mutuwo |