Masalimo 75:6 - Buku Lopatulika6 Pakuti kukuzaku sikuchokera kum'mawa, kapena kumadzulo, kapena kuchipululu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Pakuti kukuzaku sikuchokera kum'mawa, kapena kumadzulo, kapena kuchipululu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Kugamula milandu sikuchokeratu kuvuma kapena kuzambwe, ndiponso sikuchokera ku chipululu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Kugamula milandu sikuchokera kummawa kapena kumadzulo kapena ku chipululu. Onani mutuwo |