Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 75:5 - Buku Lopatulika

5 musamakwezetsa nyanga yanu; musamalankhula ndi khosi louma.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 musamakwezetsa nyanga yanu; musamalankhula ndi khosi louma.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 Musadzikuze chifukwa cha mphamvu zanu, kapena kumalankhula zamwano.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Musatukule nyanga zanu motsutsana ndi kumwamba; musayankhule ndi khosi losololoka.’ ”

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 75:5
7 Mawu Ofanana  

Musamakhala ouma khosi monga makolo anu; koma gwiranani dzanja ndi Yehova, nimulowe m'malo ake opatulika, amene anapatula kosatha, ndi kutumikira Yehova Mulungu wanu; kuti mkwiyo wake waukali utembenuke kwa inu.


Achita ufumu mwa mphamvu yake kosatha; maso ake ayang'anira amitundu; opikisana ndi Iye asadzikuze.


Ndipo Yehova anati kwa Mose, Ndawapenya anthu awa, taona, ndiwo anthu opulupudza;


Popeza ndinadziwa, kuti uli wokanika, ndi khosi lako lili mtsempha wachitsulo, ndi mphumi yako mkuwa;


Ndipo anawa, ndiwo achipongwe ndi ouma mtima, ndikutumiza kwa iwo; ndipo ukanene nao, Atero Yehova Mulungu.


Ouma khosi ndi osadulidwa mtima ndi makutu inu, mukaniza Mzimu Woyera nthawi zonse; monga anachita makolo anu, momwemo inu.


Pakuti ndidziwa kupikisana kwanu, ndi kupulukira kwanu; taonani, pokhala ndikali ndi moyo pamodzi ndi inu lero, mwapikisana ndi Yehova; koposa kotani nanga nditamwalira ine!


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa