Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 68:34 - Buku Lopatulika

34 Vomerezani kuti mphamvu nja Mulungu; ukulu wake uli pa Israele, ndi mphamvu yake m'mitambo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

34 Vomerezani kuti mphamvu nja Mulungu; ukulu wake uli pa Israele, ndi mphamvu yake m'mitambo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

34 Vomerezani kuti Mulungu ndi wamphamvu, ulamuliro wake uli pa Israele, mphamvu zake zili mu mlengalenga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

34 Lengezani za mphamvu za Mulungu, amene ulemerero wake uli pa Israeli amene mphamvu zake zili mʼmitambo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 68:34
9 Mawu Ofanana  

Aleluya. Lemekezani Mulungu m'malo ake oyera; mlemekezeni m'thambo la mphamvu yake.


Liu la Yehova ndi lamphamvu; liu la Yehova ndi lalikulukulu.


Palibe wina ngati Mulungu, Yesuruni iwe, wakuyenda wokwera pathambo, kukuthandiza, ndi pa mitambo mu ukulu wake.


Mulungu wamuyaya ndiye mokhaliramo mwako; ndi pansipo pali manja osatha. Ndipo aingitsa mdani pamaso pako, nati, Ononga.


Pakuti analandira kwa Mulungu Atate ulemu ndi ulemerero, pakumdzera Iye mau otere ochokera ku ulemerero waukulu, Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa, amene Ine ndikondwera naye;


Ndipo ndinamva ngati mau a khamu lalikulu, ngati mkokomo wa madzi ambiri, ngati mau a mabingu olimba, ndi kunena, Aleluya; pakuti achita ufumu Ambuye Mulungu wathu, Wamphamvuyonse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa