Masalimo 68:31 - Buku Lopatulika31 Akulu adzafumira ku Ejipito; Kusi adzafulumira kutambalitsa manja ake kwa Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Akulu adzafumira ku Ejipito; Kusi adzafulumira kutambalitsa manja ake kwa Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Akazembe adzabwera kuchokera ku Ejipito. A ku Etiopiya adzafulumira kugonjera Mulungu pokweza manja ao kwa Iye. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Nthumwi zidzachokera ku Igupto; Kusi adzadzipereka yekha kwa Mulungu. Onani mutuwo |
Ndipo ndidzaika chizindikiro pakati pao, ndipo ndidzatumiza onse amene apulumuka mwa iwo kwa amitundu, kwa Tarisisi, kwa Puti ndi kwa Aludi, okoka uta kwa Tubala ndi Yavani, kuzisumbu zakutali, amene sanamve mbiri yanga, ngakhale kuona ulemerero wanga; ndipo adzabukitsa ulemerero wanga pakati pa amitundu.