Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 68:26 - Buku Lopatulika

26 Lemekezani Mulungu m'misonkhano, ndiye Yehova, inu a gwero la Israele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

26 Lemekezani Mulungu m'masonkhano, ndiye Ambuye, inu a gwero la Israele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

26 “Tamandani Mulungu mu msonkhano waukulu. Tamandani Chauta, inu zidzukulu za Israele.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

26 Tamandani Mulungu mu msonkhano waukulu; tamandani Yehova mu msonkhano wa Israeli.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 68:26
10 Mawu Ofanana  

Amkwezenso mu msonkhano wa anthu, namlemekeze pokhala akulu.


Aleluya. Ndidzayamika Yehova ndi mtima wonse, mu upo wa oongoka mtima, ndi mumsonkhano.


Phazi langa liponda pachidikha, m'misonkhano ndidzalemekeza Yehova.


Ndipo oimba ndi oomba omwe adzati, akasupe anga onse ali mwa inu.


Ndipo Miriyamu mneneriyo, mlongo wa Aroni, anagwira lingaka m'dzanja lake; ndipo akazi onse anatuluka kumtsata ndi malingaka ndi kuthira mang'ombe.


Kodi magwero ako ayenera kumwazika kunja, ndi mitsinje ya madzi m'makwalala?


Imvani inu ichi, banja la Yakobo, amene mutchedwa ndi dzina la Israele, amene munatuluka m'madzi a Yuda amene mulumbira dzina la Yehova ndi kutchula dzina la Mulungu wa Israele, koma si m'zoona, pena m'chilungamo.


Ndipo Israele akhala mokhazikika pa yekha; kasupe wa Yakobo; akhala m'dziko la tirigu ndi vinyo; inde thambo lake likukha mame.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa