Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 68:22 - Buku Lopatulika

22 Ambuye anati, Ndidzawatenganso ku Basani, ndidzawatenganso kozama kwa nyanja,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Ambuye anati, Ndidzawatenganso ku Basani, ndidzawatenganso kozama kwa nyanja,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Ambuye adati, “Ndidzaŵabweza adani anu kuchokera ku Basani, ndidzaŵabweza kuchokera ku nyanja yozama,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Ambuye akunena kuti, “Ndidzawabweretsa kuchokera ku Basani; ndidzawabweretsa kuchokera ku nyanja zozama.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 68:22
11 Mawu Ofanana  

Adzaweruza mwa amitundu, adzadzaza dziko ndi mitembo; adzaphwanya mitu m'maiko ambiri.


Ndipo ana a Israele analowa pakati pa nyanja pouma; ndi madziwo anakhala kwa iwo ngati khoma palamanja, ndi palamanzere.


Koma ana a Israele anayenda pouma pakati pa nyanja; ndi madziwo anakhala ngati khoma kwa iwo, palamanja ndi lamanzere.


Atero Ambuye Yehova, Taona ndidzakodola anthu a mitundu, ndi kukwezera anthu mbendera yanga; ndipo adzabwera nao ana ako aamuna pa chifuwa chao, ndi ana ako aakazi adzatengedwa pa mapewa ao.


Pakuti ndidzakutengani kukutulutsani kwa amitundu, ndi kukusokolotsani m'maiko onse, ndi kubwera nanu m'dziko lanu.


Ndipo anatembenuka nakwera kudzera njira ya ku Basani; ndipo Ogi mfumu ya ku Basani anatuluka kukumana nao, iye ndi anthu ake onse, kudzachita nao nkhondo ku Ederei.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa