Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 68:15 - Buku Lopatulika

15 Phiri la Basani ndilo phiri la Mulungu; Phiri la Basani ndilo phiri la mitumitu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Phiri la Basani ndilo phiri la Mulungu; Phiri la Basani ndilo phiri la mitumitu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Iwe phiri la Basani, phiri laulemerero, Iwe phiri la Basani, phiri la nsonga zambiri!

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Mapiri a Basani ndi mapiri aulemerero; mapiri a Basani, ndi mapiri a msonga zambiri.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 68:15
7 Mawu Ofanana  

Koma Ine ndadzoza mfumu yanga Pa Ziyoni, phiri langa loyera.


Mudyetse anthu anu ndi ndodo yanu, nkhosa za cholowa chanu zokhala pazokha m'nkhalango pakati pa Karimele, zidye mu Basani ndi mu Giliyadi masiku a kale lomwe.


mizinda yonse ya kuchidikha, ndi Giliyadi lonse, ndi Basani lonse kufikira ku Saleka ndi Ederei, mizinda ya dziko la Ogi mu Basani.


Pamenepo Abimeleki anakwera kunka kuphiri la Zalimoni, iye ndi anthu onse anali naye; natenga nkhwangwa m'dzanja lake Abimeleki, nadula nthambi kumitengo, nainyamula ndi kuiika paphewa pake, nati kwa anthu okhala naye, Ichi munachiona ndachita, fulumirani, muchite momwemo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa