Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 65:7 - Buku Lopatulika

7 Amene atontholetsa kukuntha kwa nyanja, kukuntha kwa mafunde ake, ndi phokoso la mitundu ya anthu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Amene atontholetsa kukuntha kwa nyanja, kukuntha kwa mafunde ake, ndi phokoso la mitundu ya anthu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Inu mumachititsa bata mkokomo wa nyanja ndi mkokomo wa mafunde ndi phokoso la mitundu ina ya anthu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Amene munakhalitsa bata nyanja kukokoma kwa mafunde ake, ndi phokoso la anthu a mitundu ina.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 65:7
17 Mawu Ofanana  

Asanduliza namondwe akhale bata, kotero kuti mafunde ake atonthole.


Musaiwale mau a iwo otsutsana ndi Inu; kusokosera kwa iwo akuukirani Inu kumakwera kosaleka.


Indedi, kuzaza kwake kwa munthu kudzakulemekezani; chotsalira cha kuzazaku mudzachiletsa.


Inu ndinu wakuchita ufumu pa kudzikuza kwa nyanja; pakuuka mafunde ake muwachititsa bata.


Yehova achita ufumu; wadziveka ndi ukulu; wadziveka Yehova, wadzimangirira mphamvu m'chuuno; dziko lomwe lokhalamo anthu likhakizika, silidzagwedezeka.


Iye analenga dziko lapansi ndi mphamvu yake, nakhazikitsa dziko lapansi ndi nzeru yake, nayala thambo ndi kuzindikira kwake;


Momwemo ananyamula Yona, namponya m'nyanja; ndipo nyanja inaleka kukokoma kwake.


Koma Yehova anautsa chimphepo chachikulu panyanja, ndipo panali namondwe wamkulu panyanja, ndi chombo chikadasweka.


Ndipo m'mene anati kwa iwo, Ndine, anabwerera m'mbuyo, nagwa pansi.


Pilato anayankha, Chimene ndalemba, ndalemba.


Ndipo pamene ananena izi, anamasula msonkhano.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa