Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 65:12 - Buku Lopatulika

12 Akukha pa mabusa a m'chipululu; ndipo mapiri azingika nacho chimwemwe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Akukha pa mabusa a m'chipululu; ndipo mapiri azingika nacho chimwemwe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Ngakhale ku mabusa akuchipululu kumamera msipu wambiri, ndipo mapiri amadzazidwa ndi chimwemwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Malo a udzu a mʼchipululu amasefukira; mapiri avekedwa ndi chisangalalo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 65:12
6 Mawu Ofanana  

Ndinu amene mukhazikitsa mapiri ndi mphamvu yanu; pozingidwa nacho chilimbiko.


Musamaopa, nyama zakuthengo inu; pakuti m'chipululu muphukanso msipu; pakuti mitengo ibala zipatso zao; mikuyu ndi mipesa ipatsa mphamvu zao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa