Masalimo 65:11 - Buku Lopatulika11 Muveka chakachi ndi ukoma wanu; ndipo mabande anu akukha zakucha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Muveka chakachi ndi ukoma wanu; ndipo mabande anu akukha zakucha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Pakutha pa chaka mumapereka zokolola zambiri mwa ubwino wanu, kulikonse kumene Inu mupita, kumapezeka dzinthu dzambiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Inu mumaveka chaka ndi zinthu zochuluka, ndipo ngolo zanu zimasefukira ndi zinthu zochuluka. Onani mutuwo |