Masalimo 65:10 - Buku Lopatulika10 Mukhutitsa nthaka yake yolima; mufafaniza nthumbira zake; muiolowetsa ndi mvumbi; mudalitsa mmera wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Mukhutitsa nthaka yake yolima; mufafaniza nthumbira zake; muiolowetsa ndi mvumbi; mudalitsa mmera wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Inu mumathirira kwambiri makwaŵa am'mizere, mumasalaza nthumbira zake, mumafeŵetsa nthaka ndi mvula, ndipo mumadalitsa mbeu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Mwadzaza nthaka yake ndi madzi ndi kusalaza migula yake, mwayifewetsa ndi mvula yamawawa ndi kudalitsa mbewu zake. Onani mutuwo |