Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 63:6 - Buku Lopatulika

6 Pokumbukira Inu pa kama wanga, ndi kulingalira za Inu maulonda a usiku.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Pokumbukira Inu pa kama wanga, ndi kulingalira za Inu maulonda a usiku.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Ndikagona pabedi panga ndimalingalira za Inu, usiku wonse ndimasinkhasinkha za Inu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Pa bedi panga ndimakumbukira inu; ndimaganiza za Inu nthawi yonse ya usiku.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 63:6
12 Mawu Ofanana  

Inde akadakukopani muchoke posaukira, mulowe kuchitando kopanda chopsinja; ndipo zoikidwa pagome panu zikadakhala zonona ndithu.


Ndidzaimbira Yehova m'moyo mwanga: ndidzaimbira Mulungu wanga zomlemekeza pokhala ndilipo.


Usiku ndinakumbukira dzina lanu, Yehova, ndipo ndinasamalira chilamulo chanu.


Okondedwa ake atumphe mokondwera mu ulemu: Afuule mokondwera pamakama pao.


Koma usana Yehova adzalamulira chifundo chake, ndipo usiku nyimbo yake idzakhala ndi ine. Inde pemphero la kwa Mulungu wa moyo wanga.


Ndinagona tulo, koma mtima wanga unali maso: Ndi mau a bwenzi langa mnyamatayo agogoda, nati, nditsegulire, mlongo wanga, wokondedwa wanga, nkhunda yanga, wangwiro wanga. Pakuti pamutu panga padzala mame, patsitsi panga pali madontho a usiku.


Ndipo ndikhutitsa moyo wa ansembe ndi mafuta, ndipo anthu anga adzakhuta ndi zokoma zanga, ati Yehova.


Tauka, tafuula usiku, poyamba kulonda; tsanulira mtima wako ngati madzi pamaso pa Ambuye; takwezera maso ako kwa Iye, chifukwa cha moyo wa tiana tako, timene tilefuka ndi njala pa malekezero a makwalala onse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa