Masalimo 63:4 - Buku Lopatulika4 Potero ndidzakuyamikani m'moyo mwanga; ndidzakweza manja anga m'dzina lanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Potero ndidzakuyamikani m'moyo mwanga; ndidzakweza manja anga m'dzina lanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Choncho ndidzakutamandani masiku onse a moyo wanga. Ndidzakweza manja anga kwa Inu mopemphera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ndidzakutamandani masiku onse a moyo wanga, ndipo mʼdzina lanu ndidzakweza manja anga. Onani mutuwo |