Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 62:3 - Buku Lopatulika

3 Mudzamvumvulukira munthu mpaka liti, kumupha iye, nonsenu, monga khoma lopendekeka, ndi mpanda woweyeseka?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Mudzamvumvulukira munthu mpaka liti, kumupha iye, nonsenu, monga khoma lopendekeka, ndi mpanda woweyeseka?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Kodi nonsenu mudzaukira munthu mpaka liti, kuti mumgwetse pansi ngati khoma lopendekeka, ngati mpanda wogwedezeka?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Kodi nonsenu mudzalimbana naye munthu mpaka liti? Kodi mudzamugwetsa pansi ngati khoma losalimba, ngati mpanda wogwedezeka?

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 62:3
19 Mawu Ofanana  

Iwo akukhulupirira Yehova akunga phiri la Ziyoni, losasunthika, likhazikika kosatha.


amene adzipanga zoipa mumtima mwao; masiku onse amemeza nkhondo.


Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse; popeza ali padzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.


Ndidzaitanira Yehova, woyenera kutamandika, ndipo adzandipulumutsa ine kwa adani anga.


Pakuti anakupangirani choipa, anapangana chiwembu, osakhoza kuchichita.


Ndipo anditchera misampha iwo akufuna moyo wanga; ndipo iwo akuyesa kundichitira choipa alankhula zoononga, nalingirira zonyenga tsiku lonse.


Amuna inu, ulemu wanga udzakhala wamanyazi kufikira liti? Mudzakonda zachabe, ndi kufunafuna bodza kufikira liti?


Mudzaweruza mosalunjika kufikira liti, ndi kusamalira nkhope ya oipa?


Ndipo Mose ndi Aroni analowa kwa Farao nanena naye, Atero Yehova, Mulungu wa Ahebri, Ukana kudzichepetsa pamaso panga kufikira liti? Lola anthu anga amuke, akanditumikire;


Ndipo Yehova anati kwa Mose, Mukana kusunga zouza zanga ndi malamulo anga kufikira liti?


Kodi mudzakonda zazibwana kufikira liti, achibwana inu? Onyoza ndi kukonda kunyoza, opusa ndi kuda nzeru?


Udzagona mpaka liti, waulesi iwe? Udzauka kutulo tako liti?


Iwe Yerusalemu, utsuke mtima wako kuchotsa zoipa kuti upulumuke. Maganizo ako achabe agona mwako masiku angati?


Chinkana ndawalangiza ndi lulimbitsa manja ao, andilingiririra choipa.


Ndipo Yesu anayankha nati, Ha, obadwa osakhulupirira ndi amphulupulu, ndidzakhala ndi inu nthawi yanji? Ndidzalekerera inu nthawi yanji? Mudze naye kwa Ine kuno.


Ndipo Ayudanso anavomerezana naye, natsimikiza kuti izi zitero.


Nati Davide, Pali Yehova, Yehova adzamkantha iye; kapena tsiku la imfa yake lidzafika; kapena adzatsikira kunkhondo, nadzafako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa