Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 60:11 - Buku Lopatulika

11 Tithandizeni kunsautso; kuti chipulumutso cha munthu ndi chabe.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Tithandizeni kunsautso; kuti chipulumutso cha munthu ndi chabe.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Tithandizeni kulimbana ndi adani athuwo, pakuti chithandizo cha munthu nchopandapake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Tipatseni chithandizo kuti tilimbane ndi mdani wathu, pakuti thandizo lochokera kwa munthu ndi lopanda phindu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 60:11
8 Mawu Ofanana  

Tithandizeni mumsauko; pakuti chipulumutso cha munthu ndi chabe.


Ndipo adzaombola Israele ku mphulupulu zake zonse.


Musamakhulupirira zinduna, kapena mwana wa munthu, amene mulibe chipulumutso mwa iye.


Ombolani Israele, Mulungu, m'masautso ake onse.


Moyo wanga ukhalira chete Mulungu yekha; chipulumutso changa chifuma kwa Iye.


Pakuti thangata la Ejipito lili lachabe, lopanda pake; chifukwa chake ndamutcha Wonyada, wokhala chabe.


Koma Aejipito ndiwo anthu, si Mulungu; ndi akavalo ao ali nyama, si mzimu; ndipo pamene Yehova adzatambasula dzanja lake, wothandiza adzaphunthwa, ndi wothandizidwa adzagwa, ndipo iwo onse awiri pamodzi adzalephera.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa