Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 59:15 - Buku Lopatulika

15 Ayendeyende ndi kufuna chakudya, nachezere osakhuta.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ayendeyende ndi kufuna chakudya, nachezere osakhuta.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Amanka nafunafuna chakudya ndipo amangofuula akapanda kukhuta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Iwo amayendayenda kufuna chakudya ndipo amawuwa ngati sanakhute.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 59:15
13 Mawu Ofanana  

Ayendayenda ndi kufuna chakudya, nati, Chilikuti? Adziwa kuti lamkonzekeratu pafupi tsiku lamdima.


Ana ake akhale amchirakuyenda ndi opemphapempha; afunefune zosowa zao kuchokera m'mabwinja mwao.


Inde agalu ali osusuka, sakhuta konse; amenewa ali abusa osazindikira; iwo onse atembenukira kunjira zao, yense kutsata phindu lake m'dera lake.


Ndipo iwo adzapitirira ovutidwa ndi anjala, ndipo padzakhala kuti pokhala ndi njala iwo adzadziputa okha, ndi kutemberera mfumu yao, ndi Mulungu wao; ndi kugadamira nkhope zao kumwamba;


Timalowa m'zoopsa potenga zakudya zathu, chifukwa cha lupanga la m'chipululu.


Atero Yehova za aneneri akulakwitsa anthu anga; akuluma ndi mano ao, ndi kufuula, Mtendere; ndipo aliyense wosapereka m'kamwa mwao, amkonzera nkhondo;


chifukwa chake mudzatumikira adani anu amene Yehova adzakutumizirani, ndi njala, ndi ludzu, ndi usiwa, ndi kusowa zinthu zonse; ndipo adzaika goli lachitsulo pakhosi panu, kufikira atakuonongani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa