Masalimo 59:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo abwere madzulo, auwe ngati galu, nazungulire mzinda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo abwere madzulo, auwe ngati galu, nazungulire mudzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Amabweranso madzulo aliwonse akuuwa ngati agalu, nkumangoyendayenda mu mzinda. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Iwo amabweranso madzulo, akuchita phokoso ngati agalu ndi kumangoyenda mu mzinda. Onani mutuwo |