Masalimo 58:7 - Buku Lopatulika7 Apitetu ngati madzi oyenda; popiringidza mivi yake ikhale yodukaduka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Apitetu ngati madzi oyenda; popiringidza mivi yake ikhale yodukaduka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Azimirire ngati madzi opita, mivi yao iŵafotere m'manja ngati udzu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mulole kuti asowe ngati madzi oyenda pamene iwo akoka uta mulole kuti mivi yawo ikhale yosathwa. Onani mutuwo |