Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 58:5 - Buku Lopatulika

5 Imene siimvera liu la oitana, akuchita matsenga mochenjeratu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Imene siimvera liu la oitana, akuchita matsenga mochenjeratu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 kotero kuti siimva liwu loitana la kamatsenga, ngakhale akhale wochenjera chotani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 Imene simva liwu la munthu wamatsenga, ngakhale akhale wa luso lotani munthu wamatsengayo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 58:5
5 Mawu Ofanana  

Ndilindireni Yehova, ndisalowe m'manja mwa woipa; ndisungeni kwa munthu wachiwawa; kwa iwo akuti akankhe mapazi anga.


Ndipo mzimu wa Ejipito adzakhala wachabe pakati pake; ndipo Ine ndidzaononga uphungu wake; ndimo iwo adzafunafuna mafano ndi anyanga, ndi alauli, ndi obwebweta.


Pakuti, taonani, ndidzatumiza pa inu njoka, mphiri, zosalola kuitanidwa; ndipo zidzakulumani inu, ati Yehova.


Kapena wotsirika, kapena wobwebweta, kapena wopenduza, kapena wofunsira akufa.


Vinyo wao ndiwo ululu wa zinjoka, ndi ululu waukali wa mphiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa