Masalimo 58:10 - Buku Lopatulika10 Wolungama adzakondwera pakuona kubwezera chilango, adzasamba mapazi ake m'mwazi wa woipa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Wolungama adzakondwera pakuona kubwezera chilango, adzasamba mapazi ake m'mwazi wa woipa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Munthu wangwiro adzakondwera poona kulipsirako. Adzasamba mapazi ake m'magazi a anthu oipawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Olungama adzasangalala poona kubwezera chilango, pamene adzasambitsa mapazi awo mʼmagazi a anthu oyipa. Onani mutuwo |