Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 56:6 - Buku Lopatulika

6 Amemezana, alalira, atchereza mapazi anga, popeza alindira moyo wanga.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Amemezana, alalira, atchereza mapazi anga, popeza alindira moyo wanga.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Amasonkhana okhaokha namabisalira, amalonda mayendedwe anga, amafuna kundipha.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Iwo amakambirana, amandibisalira, amayangʼanitsitsa mayendedwe anga ndipo amakhala ndi chidwi chofuna kuchotsa moyo wanga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 56:6
22 Mawu Ofanana  

Koma tsopano muwerenga moponda mwanga; kodi simuyang'anitsa tchimo langa?


Iwo anandiyasamira pakamwa pao; anandiomba pama ndi kunditonza; asonkhana pamodzi kunditsutsa.


Nanga sapenya njira zanga, ndi kuwerenga moponda mwanga monse?


amene adzipanga zoipa mumtima mwao; masiku onse amemeza nkhondo.


Woipa aunguza wolungama, nafuna kumupha.


Ananditchera ukonde apo ndiyenda; moyo wanga wawerama. Anandikumbira mbuna patsogolo panga; anagwa m'kati mwake iwo okha.


Pakuti onani, alalira moyo wanga; amphamvu andipangira chiwembu, osachimwa, osalakwa ine, Yehova,


Pakuti adani anga alankhula za ine; ndipo iwo akulalira moyo wanga apangana upo,


Chimene adani anu, Yehova, atonza nacho; chimene atonzera nacho mayendedwe a wodzozedwa wanu.


Usabisalire, woipa iwe, pomanga wolungama; usapasule popuma iyepo.


Taona, iwo angasonkhanitse pamodzi, koma si ndi Ine; aliyense amene adzasonkhana pamodzi akangane ndi iwe adzagwa chifukwa cha iwe.


Pakuti ndamva kugogodera kwa ambiri, mantha pozungulira ponse. Neneza, ndipo tidzamneneza iye, ati atsamwali anga onse, amene ayang'anira kutsimphina kwanga; kapena adzakopedwa, ndipo ife tidzampambana iye, ndipo tidzambwezera chilango.


Ndipo akuluwa ndi akalonga anayesa kumtola chifukwa Daniele, kunena za ufumuwo; koma sanakhoze kupeza chifukwa kapena cholakwira, popeza anali wokhulupirika; ndipo saonana chosasamala kapena cholakwa chilichonse mwa iye.


Ndipo iwo akugwira Yesu ananka naye kwa Kayafa, mkulu wa ansembe, kumene adasonkhana alembi ndi akulu omwe.


Ndipo pakudza mamawa, ansembe aakulu ndi akulu a anthu onse anakhala upo wakumchitira Yesu, kuti amuphe;


Ndipo anamyang'anira, natumiza ozonda, amene anadzionetsera ngati olungama mtima, kuti akamkole pa mau ake, kotero kuti akampereke Iye ku ukulu ndi ulamuliro wa kazembe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa