Masalimo 56:12 - Buku Lopatulika12 Zowindira Inu Mulungu, zili pa ine, ndidzakuchitirani zoyamika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Zowindira Inu Mulungu, zili pa ine, ndidzakuchitirani zoyamika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Ndiyenera kuchita zimene ndidalumbira kwa Inu Mulungu. Ndidzapereka kwa Inu nsembe zothokozera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ndiyenera kuchita zomwe ndinalumbira kwa Mulungu; ndidzapereka nsembe zanga zachiyamiko kwa inu. Onani mutuwo |