Masalimo 56:11 - Buku Lopatulika11 Pa Mulungu ndakhulupirira, sindidzaopa; munthu adzandichitanji? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Pa Mulungu ndakhulupirira, sindidzaopa; munthu adzandichitanji? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Ndimadalira Mulungu, sindidzachita mantha konse. Kodi munthu angandichite chiyani? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 mwa Mulungu ine ndimadalira ndipo sindidzachita mantha. Kodi munthu angandichite chiyani? Onani mutuwo |