Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 56:10 - Buku Lopatulika

10 Mwa Mulungu ndidzalemekeza mau ake, mwa Yehova ndidzalemekeza mau ake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Mwa Mulungu ndidzalemekeza mau ake, mwa Yehova ndidzalemekeza mau ake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Ndimatamanda Mulungu chifukwa cha mau ake. Ndimatamanda Chauta chifukwa cha zimene wandilonjeza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Mwa Mulungu amene mawu ake ndimawatamanda, mwa Yehova amene mawu ake ndimawatamanda,

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 56:10
10 Mawu Ofanana  

Mundipulumutsetu ine m'dzanja la mkulu wanga, m'dzanja la Esau; chifukwa ine ndimuopa iye, kapena adzadza kudzandikantha ine, ndi amai pamodzi ndi ana.


Ndipo kunali, pamene akapitao a magaleta anaona Yehosafati, anati, Ndiye mfumu ya Israele. Potero anamtembenukira kuyambana naye; koma Yehosafati anafuula, namthandiza Yehova; ndipo Mulungu anawapatukitsa amleke.


Yehova ndi wanga; sindidzaopa; adzandichitanji munthu?


Akadapanda kukhala nafe Yehova, anene tsono Israele;


Akadapanda kukhala nafe Yehova, pakutiukira anthu:


Mwa Mulungu ndidzalemekeza mau ake, ndakhulupirira Mulungu, sindidzaopa; anthu adzandichitanji?


Mulungu walankhula m'chiyero chake; ndidzakondwerera, ndidzagawa Sekemu, ndidzayesa muyeso chigwa cha Sukoti.


Thambo ndi dziko lapansi zidzachoka, koma mau anga sadzachoka ai.


kuti mwa zinthu ziwiri zosasinthika, m'mene Mulungu sangathe kunama, tikakhale nacho chotichenjeza cholimba, ife amene tidathawira kuchigwira chiyembekezo choikika pamaso pathu;


mwa izi adatipatsa malonjezano a mtengo wake ndi aakulu ndithu; kuti mwa izi mukakhale oyanjana nao umulungu wake, mutapulumuka kuchivundi chili padziko lapansi m'chilakolako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa