Masalimo 55:16 - Buku Lopatulika16 Koma ine ndidzafuulira kwa Mulungu; ndipo Yehova adzandipulumutsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Koma ine ndidzafuulira kwa Mulungu; ndipo Yehova adzandipulumutsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Koma ine ndikupempha Chauta, ndipo Iye adzandithandiza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Koma ine ndinafuwulira kwa Mulungu, ndipo Yehova anandipulumutsa. Onani mutuwo |