Masalimo 55:12 - Buku Lopatulika12 Pakuti si mdani amene ananditonzayo; pakadatero ndikadachilola, amene anadzikuza pa ine sindiye munthu wondida; pakadatero ndikadambisalira: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Pakuti si mdani amene ananditonzayo; pakadatero ndikadachilola, amene anadzikuza pa ine sindiye munthu wondida; pakadatero ndikadambisalira: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Akadakhala mdani wanga wondinyozayo, ndikadatha kupirira. Akadakhala mdani wanga wondichita chipongweyo, ndikadangobisala basi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Akanakhala mdani akundinyoza, ine ndikanapirira; akanakhala mdani akudzikweza yekha kutsutsana nane, ndikanakabisala. Onani mutuwo |