Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 55:11 - Buku Lopatulika

11 M'kati mwake muli kusakaza, chiwawa ndi chinyengo sizichoka m'makwalala ake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 M'kati mwake muli kusakaza, chiwawa ndi chinyengo sizichoka m'makwalala ake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 M'menemo muli chiwonongeko chokhachokha. M'misika yake muli zopanikizana ndi zonyenga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Mphamvu zowononga zili pa ntchito mu mzinda; kuopseza ndi mabodza sizichoka mʼmisewu yake.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 55:11
10 Mawu Ofanana  

M'kamwa mwake mwadzala kutemberera ndi manyengo ndi kuchenjerera; pansi pa lilime lake pali chivutitso chopanda pake.


Pakuti m'kamwa mwao mulibe mau okhazikika; m'kati mwao m'mosakaza; m'mero mwao ndi manda apululu; lilime lao asyasyalika nalo.


Maukonde ao sadzakhala zovala, sadzafunda ntchito zao; ntchito zao zili ntchito zoipa, ndi chiwawa chili m'manja mwao.


Mapazi ao athamangira koipa, ndipo iwo afulumira kukhetsa mwazi wosachimwa; maganizo ao ali maganizo oipa; bwinja ndi chipasuko zili m'njira mwao.


nakhala upo wakuti amgwire Yesu ndi chinyengo, namuphe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa