Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 50:20 - Buku Lopatulika

20 Ukhala, nuneneza mbale wako; usinjirira mwana wa mai wako.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Ukhala, nuneneza mbale wako; usinjirira mwana wa mai wako.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 “Umakhala pansi nkumachitira mbale wako miseche, inde, umasinjirira mbale wako weniweni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Nthawi zonse umayankhula motsutsana ndi mʼbale wako ndipo umasinjirira mwana wa amayi ako enieni.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 50:20
9 Mawu Ofanana  

Ikhale yosalankhula milomo ya mabodza, imene imalankhula mwachipongwe pa olungama mtima, ndi kudzikuza ndi kunyoza.


Wobisa udani ali ndi milomo yonama; wonena ugogodi ndiye chitsiru.


Usamayendayenda nusinjirira mwa anthu a mtundu wako; usamatsata mwazi wa mnansi wako; Ine ndine Yehova.


Ndipo mbale adzapereka mbale wake kuimfa, ndi atate mwana wake: ndipo ana adzatsutsa akuwabala, nadzawafetsa iwo.


Odala muli inu m'mene adzanyazitsa inu, nadzazunza inu, nadzakunenerani monama zoipa zilizonse chifukwa cha Ine.


Ndipo zambiri zina anamnenera Iye, namchitira mwano.


Momwemonso akazi akhale olemekezeka, osadierekeza, odzisunga, okhulupirika m'zonse.


Momwemonso akazi okalamba akhale nao makhalidwe oyenera anthu oyera, osadierekeza, osakodwa nacho chikondi cha pavinyo, akuphunzitsa zokoma;


Ndipo ndinamva mau aakulu mu Mwamba, nanena, Tsopano zafika chipulumutso, ndi mphamvu, ndi ufumu za Mulungu wathu, ndi ulamuliro wa Khristu wake; pakuti wagwetsedwa wonenera wa abale athu, wakuwanenera pamaso pa Mulungu wathu usana ndi usiku.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa