Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 50:19 - Buku Lopatulika

19 Pakamwa pako mpochita zochimwa, ndipo lilime lako likonza chinyengo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Pakamwa pako mpochita zochimwa, ndipo lilime lako likonza chinyengo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Suwopa kulankhula zoipa pakamwa pako, lilime lako limapeka mabodza.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Umagwiritsa ntchito pakamwa pako pa zinthu zoyipa ndipo umakonza lilime lako kuchita chinyengo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 50:19
14 Mawu Ofanana  

M'kamwa mwake mwadzala kutemberera ndi manyengo ndi kuchenjerera; pansi pa lilime lake pali chivutitso chopanda pake.


Pakuti m'kamwa mwao mulibe mau okhazikika; m'kati mwao m'mosakaza; m'mero mwao ndi manda apululu; lilime lao asyasyalika nalo.


Pakuti si mdani amene ananditonzayo; pakadatero ndikadachilola, amene anadzikuza pa ine sindiye munthu wondida; pakadatero ndikadambisalira:


Pakamwa pake mposalala ngati mafuta amkaka, koma mumtima mwake munali nkhondo, mau ake ngofewa ngati mafuta oyenga, koma anali malupanga osololasolola.


Ndipo yense adzanyenga mnansi wake, osanena choonadi; aphunzitsa lilime lao kunena zonama; nadzithodwetsa kuchita zoipa.


Koma kulumbira, ndi kunama, ndi kupha, ndi kuba, ndi kuchita chigololo; aboola, ndi mwazi ukhudzana nao mwazi.


Koma amantha, ndi osakhulupirira, ndi onyansa, ndi ambanda, ndi achigololo, ndi olambira mafano, ndi onse a mabodza, cholandira chao chidzakhala m'nyanja yotentha ndi moto ndi sulufure; ndiyo imfa yachiwiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa