Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 50:11 - Buku Lopatulika

11 Ndidziwa mbalame zonse za m'mapiri, ndipo nyama zakuthengo zili ndi Ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndidziwa mbalame zonse za m'mapiri, ndipo nyama za kuthengo zili ndi Ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Mbalame zonse zamumlengalenga, zamoyo zonse zoyenda ku thengo ndi zanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Ine ndimadziwa mbalame iliyonse mʼmapiri ndiponso zolengedwa zonse zakutchire ndi zanga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 50:11
11 Mawu Ofanana  

Amkonzeratu khwangwala chakudya chake ndani, pamenepo ana ake afuulira kwa Mulungu, naulukauluka osowa chakudya?


Mbalame za mlengalenga zifatsa pamenepo, zimaimba pakati pa mitawi.


Amene apatsa zoweta chakudya chao, ana a khwangwala alikulira.


Inu zilombo zonse za m'thengo, idzani kulusa, inde zilombo inu nonse za m'nkhalango.


Yang'anirani mbalame za kumwamba, kuti sizimafesa ai, kapena sizimatema ai, kapena sizimatutira m'nkhokwe; ndipo Atate wanu wa Kumwamba azidyetsa. Nanga inu mulibe kusiyana nazo kuziposa kodi?


Lingirirani makwangwala, kuti samafesai, kapena kutemai; alibe nyumba yosungiramo, kapena nkhokwe; ndipo Mulungu awadyetsa; nanga inu simuziposa mbalame kwambiri!


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa