Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 49:20 - Buku Lopatulika

20 Munthu waulemu, koma wosadziwitsa, afanana ndi nyama zakuthengo, afanana nazo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Munthu waulemu, koma wosadziwitsa, afanana ndi nyama za kuthengo, afanana nazo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Ngakhale munthu akhale wolemera chotani, komabe akasoŵa nzeru, adzafa chabe ngati nyama zakuthengo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Munthu amene ali ndi chuma koma wopanda nzeru adzafa ngati nyama yakuthengo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 49:20
8 Mawu Ofanana  

Nampachika Hamani pa mtengo adaukonzera Mordekai. Pamenepo mkwiyo wa mfumu unatsika.


ndisanachoke kunka kumene sindikabweranso, ku dziko la mdima ndi la mthunzi wa imfa.


Kukometsetsa kwao sikumachotsedwa nao? Amafa koma opanda nzeru.


Koma munthu wa ulemu wake sakhalitsa, afanana ndi nyama zakuthengo, afanana nazo.


Inde, munthu akakhala ndi moyo zaka zambiri, akondwere ndi zonsezo; koma akumbukire masiku amdima kuti adzachuluka. Zonse zilinkudza zili zachabe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa