Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 49:19 - Buku Lopatulika

19 Adzamuka kumbadwo wa makolo ake; sadzaona kuunika nthawi zonse.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Adzamuka kumbadwo wa makolo ake; sadzaona kuunika nthawi zonse.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 adzafabe nkukakumana ndi makolo ake onse kumanda, kumene sadzaona kuŵala mpaka muyaya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 iyeyo adzakakhala pamodzi ndi mʼbado wa makolo ake, amene sadzaonanso kuwala.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 49:19
11 Mawu Ofanana  

Ndipo iwe udzanka kwa makolo ako m'mtendere; nudzaikidwa ndi ukalamba wabwino.


Nagona Baasa ndi makolo ake, naikidwa ku Tiriza; ndipo Ela mwana wake analowa ufumu m'malo mwake.


kumbweza angalowe kumanda, kuti kuunika kwa moyo kumuwalire.


Pakuti mwalanditsa moyo wanga kuimfa, simunatero nao mapazi anga kuti ndingagwe? Kuti ndiyende pamaso pa Mulungu m'kuunika kwa amoyo.


fumbi ndi kubwera pansi pomwe linali kale, mzimu ndi kubwera kwa Mulungu amene anaupereka.


Ndani adziwa mzimu wa ana a anthu wokwera kumwamba, ndi mzimu wa nyama wotsikira kunsi ku dziko?


Pomwepo mfumu inati kwa atumiki, Mumange iye manja ndi miyendo, mumponye kumdima wakunja; komweko kudzali kulira ndi kukukuta mano.


koma anawo a Ufumu adzatayidwa kumdima wakunja; komweko kudzakhala kulira ndi kukukuta mano.


Koma Mulungu anati kwa iye, Wopusa iwe, usiku womwe uno udzafunidwa moyo wako; ndipo zinthu zimene unazikonza zidzakhala za yani?


mafunde oopsa a nyanja, akuwinduka thovu la manyazi a iwo okha; nyenyezi zosokera, zimene mdima wakuda bii udazisungikira kosatha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa